99. Az-Zalzala
1Pamene dziko lidzagwedezeka ndi chivomerezi chomaliza
2Ndipo pamene nthaka idzatulutsa katundu amene ali m’kati mwake
3Ndipo munthu adzafunsa: “Kodi yatani?”
4Pa tsikuli nthaka idzaulula zonse
5Chifukwa Ambuye wako wayiuza kuti itero
6Pa tsikuli mtundu wa anthu udzadza m’magulu osiyana siyana kudzalangizidwa ntchito zawo
7Motero aliyense amene amachita chabwino cholemera ngati njere ya mpiru, adzachiona
8Ndipo aliyense amene amachita choipa cholemera ngati njere ya mpiru, adzachiona
WEBREATH · 11:11
«If you are thankful, I will give you more» — Quran 14:7
Breath is one for all: everyone lives by it, whoever they are and whatever they believe. Every day at 11:11 local time people stop for sixty seconds, breathe, and thank GOD for the breath — each in their own words, each within themselves. In that minute we are One Breath.
WEBREATH — the Minute at 11:11, your own local time — we are One Breath