Chisilamu
kubwerera

113. Al-Falaq

1Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa M’mbandakucha

2Kuchokera ku zinthu zonyansa zimene walenga

3Ndi kuchokera ku zonyansa za nthawi ya usiku pamene mdima ufika

4Ndi kuchokera ku zonyansa za anthu a matsenga pamene auzila pfundo

5“Ndi ku zonyansa za munthu wa dumbo pamene achita nsanje.”

gwero: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

WEBREATH · 11:11

«If you are thankful, I will give you more» — Quran 14:7

Breath is one for all: everyone lives by it, whoever they are and whatever they believe. Every day at 11:11 local time people stop for sixty seconds, breathe, and thank GOD for the breath — each in their own words, each within themselves. In that minute we are One Breath.

WEBREATH — the Minute at 11:11, your own local time — we are One Breath