Chisilamu
kubwerera

107. Al-Maa'un

1Kodi wamuona munthu amene amakana kuti kuli tsiku la chiweruzo

2Iye ndiye amene amazunza mwana wamasiye

3Ndipo sakakamiza anthu ena kuti azidyetsa anthu osauka

4Motero tsoka kwa iwo amene amapemphera

5Amene salabadira mapemphero awo

6Amene amachita zabwino pofuna kuti ena awaone

7Ndipo amakana kupereka chaulere

gwero: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

WEBREATH · 11:11

«If you are thankful, I will give you more» — Quran 14:7

Breath is one for all: everyone lives by it, whoever they are and whatever they believe. Every day at 11:11 local time people stop for sixty seconds, breathe, and thank GOD for the breath — each in their own words, each within themselves. In that minute we are One Breath.

WEBREATH — the Minute at 11:11, your own local time — we are One Breath