Chisilamu
kubwerera

106. Quraish

1Pofuna kuteteza mtundu wa Quraish

2Kuti apitirire pa maulendo nthawi ya Chilimwe ndi m’nthawi ya Chisanu

3Motero auzeni kuti azipembedza Ambuye wa Nyumba ino

4Amene wawadyetsa m’masiku a njala ndi kuwachotsa mantha

gwero: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

WEBREATH · 11:11

«If you are thankful, I will give you more» — Quran 14:7

Breath is one for all: everyone lives by it, whoever they are and whatever they believe. Every day at 11:11 local time people stop for sixty seconds, breathe, and thank GOD for the breath — each in their own words, each within themselves. In that minute we are One Breath.

WEBREATH — the Minute at 11:11, your own local time — we are One Breath