Chisilamu
kubwerera

100. Al-Aadiyaat

1Palizothamangakwambirindikupumakwawokofulumira

2Ndi zimene zimaonetsa moto zikamathamanga

3Ndipo zimachita nkhondo m’mbandakucha

4Ndi kuonetsa fumbi

5Ndi kuphwanya pakati gulu la adani

6Ndithudi! Munthu sathokoza kwaAmbuye wake

7Ndipo mwini wake amachitira umboni zimenezi

8Ndithudi iye ali kukonda chuma kwambiri

9Kodi iye sadziwa kuti pamene zonse zili m’manda zidzatulutsidwa ndi kuonetsedwa poyera

10Ndizonsezimenezilim’mitimayaanthuzizidzaululidwa

11Ndithudi, patsiku limeneli, Ambuye wako adzakhala ali kudziwa chilichonse

gwero: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

WEBREATH · 11:11

«If you are thankful, I will give you more» — Quran 14:7

Breath is one for all: everyone lives by it, whoever they are and whatever they believe. Every day at 11:11 local time people stop for sixty seconds, breathe, and thank GOD for the breath — each in their own words, each within themselves. In that minute we are One Breath.

WEBREATH — the Minute at 11:11, your own local time — we are One Breath